Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 7:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tikati, Tilowe m'mudzi, m'mudzi muli njala, tidzafa m'mwemo; tikakhala pompano, tidzafanso. Tiyeni tsono, tigwe ku misasa ya Aaramu; akatisunga ndi moyo, tidzakhala ndi moyo; akatipha, tangokufa.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 7

Onani 2 Mafumu 7:4 nkhani