Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 7:19-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

19. ndipo kazembe uja adayankha munthu wa Mulunguyo, nati, Taonani tsono, Yehova angacite mazenera m'mwamba, cikacitika ici kodi? Nati iye, Taona, udzaciona ici ndi maso ako, koma osadyako ai;

20. kudamcitikira momwemo; popeza anthu anampondereza pacipata nafa iye.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 7