Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 6:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati munthu wa Mulungu, Yagwera pati? Namuonetsapo yagwera. Pamenepo anadula kamtengo, nakaponya pomwepo, nayandamitsa nkhwangwayo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 6

Onani 2 Mafumu 6:6 nkhani