Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 6:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nanena naye mfumu, Ufunanji? Nati iye, Mnzanga uyu ananena ndi ine, Tenga mwana wako timudye lero, ndi mwana wanga timudye mawa.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 6

Onani 2 Mafumu 6:28 nkhani