Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 6:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma m'Samariya munali njala yaikuru; ndipo taonani, anaumangira misasa mpaka mutu wa buru unagulidwa ndalama zasiliva makumi asanu ndi atatu; ndi limodzi la magawo anai la muyeso wa zitosi za nkhunda linagulidwa ndi ndalama zasiliva zisanu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 6

Onani 2 Mafumu 6:25 nkhani