Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 6:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo atatsikira pali iye, Elisa anapemphera kwa Yehova, nati, Mukanthe mtundu uwu ucite khungu. Ndipo iye anawakantha, nawacititsa khungu, monga mwa mau a Elisa.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 6

Onani 2 Mafumu 6:18 nkhani