Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 5:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati Namani, Viole ulandire matalente awiri. Namkangamiza namanga matalente awiri a siliva m'matumba awiri, ndi zobvala zosintha ziwiri, nasenzetsa anyamata ace awiri; iwo anatsogola atazisenza.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 5

Onani 2 Mafumu 5:23 nkhani