Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 4:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anagawira anthu kuti adye. Koma kunali; pakudya cakudyaco, anapfuula nati, Munthu wa Mulungu, muli imfa m'nkhalimo. Ndipo sanatha kudyako.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 4

Onani 2 Mafumu 4:40 nkhani