Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 4:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nakwera, nagona pa mwanayo ndi kulinganiza pakamwa pace ndi pakamwa pace, maso ace ndi maso ace, zikhato zace ndi zikhato zace, nadzitambasula pa iye, ndi mnofu wa mwana unafunda.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 4

Onani 2 Mafumu 4:34 nkhani