Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 4:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anati kwa Gehazi, Udzimangire m'cuuno, nutenge ndodo yanga m'dzanja lako, numuke; ukakomana ndi munthu usamlankhule; akakulankhula wina usamyankhe; ukaike ndodo yanga pankhope pa mwanayo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 4

Onani 2 Mafumu 4:29 nkhani