Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 4:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pofika kwa munthu wa Mulungu kuphiri anamgwira mapazi. Ndipo Gehazi anayandikira kuti amkankhe; koma munthu wa Mulungu anati, Umleke, pakuti mtima wace ulikumwawa; ndipo Yehova wandibisira osandiuza ici.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 4

Onani 2 Mafumu 4:27 nkhani