Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 4:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potero anamuka, nafika kwa munthu wa Mulungu ku phiri la Karimeli. Ndipo kunali, pakumuona munthu wa Mulungu alinkudza kutali, anati kwa Gehazi mnyamata wace, Tapenya, suyo Msunemu uja;

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 4

Onani 2 Mafumu 4:25 nkhani