Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 4:18-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

18. Ndipo atakula mwanayo, linadza tsiku lakuti anaturuka kumka kwa atate wace, ali kwa omweta tirigu.

19. Natikwa atate wace, Mutu wanga, mutu wanga! Pamenepo anati kwa mnyamata, Umnyamule umuke naye kwa amace.

20. Namnyamula, napita naye kwa amace. Ndipo anakhala pa maondo ace kufikira usana, namwalira.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 4