Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 4:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati kwa iye, Ufunse mkaziyu tsopano, kuti, Taona watisungira ndi kusamalira uku konse; nanga tikucitire iwe ciani? Kodi tikunenere kwa mfumu, kapena kwa kazembe wa nkhondo? Koma anati, Ndikhala ine pakati pa anthu a mtundu wanga.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 4

Onani 2 Mafumu 4:13 nkhani