Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 3:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nakatumiza mau kwa Yehosafati mfumu ya Yuda, ndi kuti, Mfumu ya Moabu wapandukana ndi ine; kodi udzamuka nane kukathira nkhondo pa Moabu? Nati, Ndidzakwera: ine ndikhala ngati iwe, anthu anga ngati anthu ako, akavalo anga ngati akavalo ako.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 3

Onani 2 Mafumu 3:7 nkhani