Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 25:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mwezi wacisanu, tsiku lacisanu ndi ciwiri la mweziwo, ndico caka cakhumi mphambu cisanu ndi cinai ca mfumu Nebukadinezara mfumu ya Babulo, Nebuzaradani mkuru wa olindirira, ndiye mnyamata wa mfumu ya Babulo, anadza ku Yerusalemu,

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 25

Onani 2 Mafumu 25:8 nkhani