Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 25:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali caka ca makumi atatu mphambu zisanu ndi ziwiri ca kumtenga ndende Yoyakini mfumu ya Yuda, mwezi wakhumi ndi ziwiri, tsiku la makumi awiri mphambu asanu ndi awiri la mwezi, Evili Merodaki mfumu ya Babulo anamuweramutsa mutu wace wa Yoyakini mfumu ya Yuda aturuke m'kaidi, caka colowa iye ufumu wace;

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 25

Onani 2 Mafumu 25:27 nkhani