Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 25:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi anthu otsalira m'mudzi, ndi opanduka akuthawira kwa mfumu ya Babulo, ndi aunyinji otsalira, Nebuzaradani mkuru wa olindirira anamuka nao andende.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 25

Onani 2 Mafumu 25:11 nkhani