Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 24:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo Yoyakini mfumu ya Yuda anaturukira kwa mfumu ya Babulo, iye ndi mace, ndi anyamata ace, ndi akalonga ace, ndi adindo ace; mfumu ya Babulo nimtenga caka cacisanu ndi citatu ca ufumu wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 24

Onani 2 Mafumu 24:12 nkhani