Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 23:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Naturutsa ansembe onse m'midzi ya Yuda, nawaipitsira misanje, imene ansembe adafukizapo zonunkhira, kuyambira Geba kufikira Beereseba; napasula misanje ya kuzipata, yokhala polowera pa cipata ca Yoswa kazembe wa mudzi, yokhala ku dzanja lako lamanzere kwa cipata ca mudzi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 23

Onani 2 Mafumu 23:8 nkhani