Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 23:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Masiku ace Farao-Neko mfumu ya Aigupto anakwerera mfumu ya Asuri ku mtsinje wa Firate; Ddipo mfumu Yosiya anaturuka kuponyana naye, koma anapha Yosiya ku Megido, atamuona.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 23

Onani 2 Mafumu 23:29 nkhani