Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 23:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo asanabadwe iye panalibe mfumu wolingana naye, imene inatembenukira kwa Yehova ndi mtima wace wonse, ndi moyo wace wonse, ndi mphamvu yace yonse, monga mwa cilamulo conse ca Mose; atafa iyeyu sanaukanso wina wolingana naye.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 23

Onani 2 Mafumu 23:25 nkhani