Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 23:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi nyumba zonse zoo mwe za ku misanje yokhala m'midzi ya Samariya, adazimanga mafumu a Israyeli kuutsa nazo mkwiyo wa Yehova, Yosiya anazicotsa, nazicitira monga mwa nchito zonse adazicita ku Beteli.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 23

Onani 2 Mafumu 23:19 nkhani