Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 23:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi maguwa a nsembe anali patsindwi pa cipinda cosanja ca Ahazi adawapanga mafumu a Yuda, ndi maguwa a nsembe adawapanga Manase m'mabwalo awiri a nyumba ya Yehova, mfumu inawagumula, niwacotsa komweko, nitaya pfumbi lao ku mtsinje wa Kidroni.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 23

Onani 2 Mafumu 23:12 nkhani