Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 22:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kwera kwa Hilikiya mkulu wa ansembe, awerenge ndalama zimene anthu anabwera nazo ku nyumba ya Yehova, ndizo zimene olindira pakhomo anasonkhetsa anthu; azipereke m'dzanja anchito akuyang'anira nyumba ya Yehova;

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 22

Onani 2 Mafumu 22:4 nkhani