Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 22:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mukani, funsirani ine, ndi anthu, ndi Yuda yense, kwa Yehova za mau a buku ili adalipeza; pakuti mkwiyo wa Yehova wotiyakira ife ndi waukuru; popeza atate athu sanamvera mau a buku ili, kucita monga mwa zonse zotilemberamo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 22

Onani 2 Mafumu 22:13 nkhani