Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 21:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaika cifanizo cosema cimene adacipanga m'nyumba ija Yehova adainenera kwa Davide ndi kwa Solomo mwana wace kuti, M'nyumba muno ndi m'Yerusalemu umene ndausankha mwa mafuko onse a Israyeli ndidzaikamo dzina langa kosatha.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 21

Onani 2 Mafumu 21:7 nkhani