Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 21:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nagona Manase ndi makolo ace, naikidwa m'munda wa nyumba yace, m'munda wa Uza, nakhala mfumu m'malo mwace Amoni mwana wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 21

Onani 2 Mafumu 21:18 nkhani