Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 21:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzayesa pa Yerusalemu cingwe coongolera ca Samariya, ndi cingwe colungamitsira ciriri ca nyumba ya Ahabu; ndidzapukuta Yerusalemu monga umo apukutira mbale, kuipukuta ndi kuibvundikira.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 21

Onani 2 Mafumu 21:13 nkhani