Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 20:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati Yesaya, Cizindikilo ndici akupatsa Yehova, kuti Yehova adzacicita conena iye; kodi mthunzi umuke m'tsogolo makwerero khumi, kapena ubwerere m'mbuyo makwerero khumi?

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 20

Onani 2 Mafumu 20:9 nkhani