Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 20:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mukumbukile Yehova kuti ndinayendabe pamaso panu m'coonadi, ndi mtima wangwiro, ndi kucita zokoma m'kuona kwanu. Nalira Hezekiya kulira kwakukuru.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 20

Onani 2 Mafumu 20:3 nkhani