Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 20:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Masiku ajawo Hezekiya anadwala, nafuna kufa. Namdzera Yesaya mneneri mwana wa Amozi, nanena naye, Atero Yehova, Siyira banja lako; pakuti udzafa, sudzakhala ndi moyo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 20

Onani 2 Mafumu 20:1 nkhani