Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 2:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali ataoloka, Eliya anati kwa Elisa, Tapempha cimene ndikucitire ndisanacotsedwe kwa iwe. Ndipo Elisa anati, Mundipatse magawo awiri a mzimu wanu akhale pa ine.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2

Onani 2 Mafumu 2:9 nkhani