Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 2:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Eliya ananena naye, Ukhale pompano, pakuti Yehova wandituma ku Yordano, Nati iye, Pali Mulungu, pali inu, sindikusiyani. Napitirira iwo awiri.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2

Onani 2 Mafumu 2:6 nkhani