Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 2:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Eliya anati kwa iye, Elisa, ukhale pompano, pakuti Yehova wandituma ku Yeriko. Nati iye, Pali Yehova, pali inu, sindikusiyani. Motero anadza ku Yeriko.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2

Onani 2 Mafumu 2:4 nkhani