Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 2:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaturuka kumka ku magwero a madzi, nathiramo mcere, nati, Atero Yehova, Ndaciritsa madzi awa, sikudzafumirakonso imfa, kapena kusabalitsa.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2

Onani 2 Mafumu 2:21 nkhani