Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 2:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Eliya anati kwa Elisa, Ukhale pompano pakuti Yehova wandituma ndimke ku Beteli. Nati Elisa, Pali Mulungu, pali inu, sindikusiyani. Motero anatsikira iwo ku Beteli.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2

Onani 2 Mafumu 2:2 nkhani