Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 2:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene anampenya ana a aneneri okhala ku Yeriko pandunji pace, anati, Mzimu wa Eliya watera pa Elisa. Ndipo anadza kukomana naye, nadziweramitsa pansi kumaso kwace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2

Onani 2 Mafumu 2:15 nkhani