Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 2:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Elisa anapenya, napfuula, Atate wanga, atate wanga, gareta wa Israyeli ndi apakavalo ace! Koma analibe kumpenyanso; nagwira zobvala zace zace, nazing'amba pakati.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 2

Onani 2 Mafumu 2:12 nkhani