Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 19:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa ca kundizazira kwako, ndi popeza kudzikuza kwako kwandifikira m'makutu mwanga, ndidzakukowa ndi ngowe yanga m'mphuno mwako, ndi cam'kamwa canga m'milomo mwako; ndipo ndidzakubwezera pa njira unadzerayi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 19

Onani 2 Mafumu 19:28 nkhani