Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 19:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Yesaya mwana wa Amozi anatumiza kwa Hezekiya, ndi, kuti, Atero Yehova Mulungu wa Israyeli, Condipempha iwe pa Sanakeribu mfumu ya Asuri ndacimva.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 19

Onani 2 Mafumu 19:20 nkhani