Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 18:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Natumiza Hezekiya mfumu ya Yuda kwa mfumu ya Asuri ku Lakisi, ndi kuti, Ndalakwa; mundicokere; cimene mundisenzetse ndisenza. Pamenepo mfumu ya Asuri anaikira Hezekiya mfumu ya Yuda matalente mazana atatu a siliva ndi matalente makumi atatu a golidi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 18

Onani 2 Mafumu 18:14 nkhani