Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 17:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Caka cacisanu ndi cinai ca Hoseya mfumu ya Asuri analanda Samariya, natenga Aisrayeli andende, kumka nao ku Asuri; nawakhalitsa m'Hala, ndi m'Habori, ku mtsinje wa Gozani, ndi m'midzi ya Amedi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 17

Onani 2 Mafumu 17:6 nkhani