Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 17:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mfumu ya Asuri anampeza Hoseya alikucita ciwembu; popeza anatuma mithenga kwa So mfumu ya ku Aigupto, osaperekanso mtulo kwa mfumu ya Asuri, monga akacita caka ndi caka; cifukwa cace mfumu ya Asuri anamtsekera, nammanga m'kaidi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 17

Onani 2 Mafumu 17:4 nkhani