Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 17:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anasiya malamulo onse a Yehova Mulungu wao, nadzipangira mafano oyenga, ana a ng'ombe awiri, napanga cifanizo, nagwadira khamu lonse la kuthambo, natumikira Baala.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 17

Onani 2 Mafumu 17:16 nkhani