Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 17:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anacitira umboni Israyeli ndi Yuda mwa dzanja la mneneri ali yense, ndi mlauli ali yense, ndi kuti, Bwererani kuleka nchito zanu zoipa, nimusunge malamulo anga ndi malemba anga, monga mwa cilamulo conse ndinacilamulira makolo anu, ndi kucitumizira inu mwa dzanja la atumiki anga aneneri.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 17

Onani 2 Mafumu 17:13 nkhani