Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 16:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Rezini mfumu ya Aramu, ndi Peka mwana wa Remaliya mfumu ya Israyeli, anakwera kumka ku Yerusalemu kukacita nkhondo, nammangira Ahazi misasa; koma sanakhoza kumgonjetsa.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 16

Onani 2 Mafumu 16:5 nkhani