Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 15:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Menahemu anasonkhetsa Israyeli ndaramazi, nasonkhetsa acuma, yense masekeli makumi asanu a siliva: kuti azipereke kwa mfumu ya Asuri. Nabwerera mfumu ya Asuri osakhala m'dzikomo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 15

Onani 2 Mafumu 15:20 nkhani