Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 14:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma ana a ambandawo sanawapha, monga mwalembedwa m'buku la cilamulo ca Mose, m'mene adalamulira Yehova, ndi kuti, Atate asaphedwere ana, kapena ana kuphedwera atate; koma yense afere kulak wa kwa iye yekha.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 14

Onani 2 Mafumu 14:6 nkhani