Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 13:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mfumu ya Aramu sanasiyira Yoahazi anthu, koma apakavalo makumi asanu, ndi magareta khumi, ndi oyenda pansi zikwi khumi; popeza mfumu ya Aramu anawaononga, nawayesa ngati pfumbi lopondapo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 13

Onani 2 Mafumu 13:7 nkhani